Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 3:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ndikunenetsa kuti, ndidzakuchotsani mu nsautso+ ya Aiguputo ndi kukulowetsani m’dziko la Akanani, Ahiti, Aamori,+ Aperizi, Ahivi, ndi Ayebusi,+ dziko loyenda mkaka ndi uchi.”’+

  • Ekisodo 13:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ndipo Yehova akadzakulowetsani m’dziko la Akanani, Ahiti, Aamori, Ahivi ndi Ayebusi,+ dziko loyenda mkaka ndi uchi,+ limene analumbirira makolo anu kuti adzakupatsani,+ pamenepo muzidzachita mwambo uwu m’mwezi uno.

  • Deuteronomo 8:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 dziko la tirigu, balere, mphesa, nkhuyu ndi makangaza,*+ dziko la maolivi opangira mafuta ndiponso la uchi,+

  • Yeremiya 2:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Pita, ukafuule m’makutu a anthu a ku Yerusalemu kuti, ‘Yehova wanena kuti:+ “Ndikukumbukira bwino kwambiri kukoma mtima kosatha kumene unali nako pamene unali wachinyamata,+ chikondi chimene unali nacho pa nthawi imene unali kulonjezedwa kukwatiwa,+ ndi kuti unanditsatira poyenda m’chipululu, m’dziko losabzalidwa kalikonse.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena