Salimo 106:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Nthawi zambiri anali kuwalanditsa,+Koma iwo anali kumupandukira chifukwa sanali kumumvera,+Ndipo anali kuwatsitsa chifukwa cha zolakwa zawo.+ 1 Akorinto 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kapena tisamuyese Yehova,+ mmene ena mwa iwo anamuyesera,+ n’kuwonongeka polumidwa ndi njoka.+
43 Nthawi zambiri anali kuwalanditsa,+Koma iwo anali kumupandukira chifukwa sanali kumumvera,+Ndipo anali kuwatsitsa chifukwa cha zolakwa zawo.+