Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yohane 3:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ndiponso, monga mmene Mose anakwezera njoka m’mwamba+ m’chipululu, momwemonso Mwana wa munthu ayenera kukwezedwa m’mwamba,+

  • Yohane 3:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 kuti aliyense wokhulupirira iye akhale nawo moyo wosatha.+

  • Yohane 6:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Pakuti chifuniro cha Atate wanga ndi chakuti, aliyense woona Mwana ndi kukhulupirira mwa iye akhale nawo moyo wosatha,+ ndipo ine ndidzamuukitsa pa tsiku lomaliza.”+

  • Aroma 1:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Mu uthenga wabwinowu, chilungamo+ cha Mulungu chimaululidwa chifukwa cha chikhulupiriro cha munthu.+ Zikatero, chikhulupiriro cha munthuyo chimalimbanso monga mmene Malemba amanenera kuti: “Koma wolungama adzakhala ndi moyo mwa chikhulupiriro chake.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena