Miyambo 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Wolungama amasamalira moyo wa chiweto chake,+ koma chisamaliro cha anthu oipa n’chankhanza.+