Numeri 22:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndithu ndidzakupatsani ulemerero waukulu,+ ndipo chilichonse chimene mungandiuze ndidzachita.+ Chonde tabwerani mudzanditembererere anthuwa.’” Numeri 24:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choka! Nyamuka uzipita. Ine ndimati ndikupatse ulemerero,+ koma taona! Yehova wakumanitsa ulemererowo.”
17 Ndithu ndidzakupatsani ulemerero waukulu,+ ndipo chilichonse chimene mungandiuze ndidzachita.+ Chonde tabwerani mudzanditembererere anthuwa.’”
11 Choka! Nyamuka uzipita. Ine ndimati ndikupatse ulemerero,+ koma taona! Yehova wakumanitsa ulemererowo.”