Numeri 23:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Nthawi yomweyo Balaki anachita monga momwe anamuuzira Balamu. Kenako, Balaki ndi Balamu anapereka nsembe. Anapereka ng’ombe yamphongo ndi nkhosa yamphongo paguwa lililonse.+
2 Nthawi yomweyo Balaki anachita monga momwe anamuuzira Balamu. Kenako, Balaki ndi Balamu anapereka nsembe. Anapereka ng’ombe yamphongo ndi nkhosa yamphongo paguwa lililonse.+