Numeri 23:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno Balamu anauza Balaki kuti: “Muime pafupi ndi nsembe yanu yopsereza.+ Mundilole ine ndichoke, kuti mwina Yehova akumana nane n’kundilankhula.+ Akatero, zimene andiuzezo n’zimenenso ndinene kwa inu.” Chotero Balamu anapita pamwamba pa phiri.
3 Ndiyeno Balamu anauza Balaki kuti: “Muime pafupi ndi nsembe yanu yopsereza.+ Mundilole ine ndichoke, kuti mwina Yehova akumana nane n’kundilankhula.+ Akatero, zimene andiuzezo n’zimenenso ndinene kwa inu.” Chotero Balamu anapita pamwamba pa phiri.