Numeri 23:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kumeneko Yehova analankhuladi ndi Balamu, n’kumuika mawu m’kamwa, ndipo anamuuza kuti:+ “Bwerera kwa Balaki+ ukamuuze zimenezi.” Numeri 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Balamu ataona kuti Yehova akungowadalitsa Aisiraeli, sanapitenso kukawafunira tsoka lina lililonse+ mmene anachitira nthawi zina zija.+ M’malomwake, anatembenuka n’kuyang’ana kuchipululu.
16 Kumeneko Yehova analankhuladi ndi Balamu, n’kumuika mawu m’kamwa, ndipo anamuuza kuti:+ “Bwerera kwa Balaki+ ukamuuze zimenezi.”
24 Balamu ataona kuti Yehova akungowadalitsa Aisiraeli, sanapitenso kukawafunira tsoka lina lililonse+ mmene anachitira nthawi zina zija.+ M’malomwake, anatembenuka n’kuyang’ana kuchipululu.