Numeri 22:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Koma mngelo wa Yehovayo anauza Balamu kuti: “Pita nawo limodzi anthuwa,+ koma ukanene zokhazo zimene ndikuuze.”+ Choncho Balamu anapitiriza ulendo wake limodzi ndi akalonga a Balakiwo. Numeri 23:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamenepo Yehova anamuika Balamu+ mawu m’kamwa, n’kumuuza kuti: “Bwerera kwa Balaki, ukamuuze mawu amenewa.”+ Numeri 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Balamu ataona kuti Yehova akungowadalitsa Aisiraeli, sanapitenso kukawafunira tsoka lina lililonse+ mmene anachitira nthawi zina zija.+ M’malomwake, anatembenuka n’kuyang’ana kuchipululu.
35 Koma mngelo wa Yehovayo anauza Balamu kuti: “Pita nawo limodzi anthuwa,+ koma ukanene zokhazo zimene ndikuuze.”+ Choncho Balamu anapitiriza ulendo wake limodzi ndi akalonga a Balakiwo.
5 Pamenepo Yehova anamuika Balamu+ mawu m’kamwa, n’kumuuza kuti: “Bwerera kwa Balaki, ukamuuze mawu amenewa.”+
24 Balamu ataona kuti Yehova akungowadalitsa Aisiraeli, sanapitenso kukawafunira tsoka lina lililonse+ mmene anachitira nthawi zina zija.+ M’malomwake, anatembenuka n’kuyang’ana kuchipululu.