Salimo 37:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Ona munthu wosalakwa ndipo yang’anitsitsa munthu wolungama,+Pakuti tsogolo la munthu ameneyu ndi lamtendere.+ Salimo 116:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 M’maso mwa YehovaImfa ya anthu ake okhulupirika ndi nkhani yaikulu.+ Miyambo 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu akamakumbukira zabwino zimene munthu wolungama anali kuchita, amam’dalitsa,+ koma dzina la anthu oipa lidzawola.+
37 Ona munthu wosalakwa ndipo yang’anitsitsa munthu wolungama,+Pakuti tsogolo la munthu ameneyu ndi lamtendere.+
7 Anthu akamakumbukira zabwino zimene munthu wolungama anali kuchita, amam’dalitsa,+ koma dzina la anthu oipa lidzawola.+