Levitiko 23:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Muziperekanso mwana wa mbuzi mmodzi+ monga nsembe yamachimo, ndi ana a nkhosa amphongo awiri, aliyense wachaka chimodzi, monga nsembe yachiyanjano.+ Numeri 28:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Muziperekanso mwana wa mbuzi+ monga nsembe yamachimo kwa Yehova, kuwonjezera pa nsembe yopsereza ya tsiku ndi tsiku, limodzi ndi nsembe yake yachakumwa.+
19 Muziperekanso mwana wa mbuzi mmodzi+ monga nsembe yamachimo, ndi ana a nkhosa amphongo awiri, aliyense wachaka chimodzi, monga nsembe yachiyanjano.+
15 Muziperekanso mwana wa mbuzi+ monga nsembe yamachimo kwa Yehova, kuwonjezera pa nsembe yopsereza ya tsiku ndi tsiku, limodzi ndi nsembe yake yachakumwa.+