Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 26:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Upange nsalu za ubweya wa mbuzi+ zoyala pachihema chopatulika. Upange nsalu 11.

  • Ekisodo 35:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Zinthu zimenezo ndizo chihema chopatulika ndi chophimba chake, ngowe zake, mafelemu ake, mipiringidzo yake, nsanamira zake ndi zitsulo zake zokhazikapo mafelemu ndi mizati.

  • Numeri 4:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Azinyamula nsalu za chihema chopatulika+ ndi chihema chokumanako,+ ndiponso chophimba chake,+ chophimba cha chikopa cha katumbu+ chomwe chili pamwamba pake, ndi nsalu yotchinga+ pakhomo la chihema chokumanako.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena