Maliko 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mwachitsanzo, Mose ananena kuti, ‘Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako,’+ komanso anati, ‘Aliyense wonenera bambo ake kapena mayi ake zachipongwe afe ndithu.’+ Aefeso 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ananu, muzimvera makolo anu+ mwa+ Ambuye, pakuti kuchita zimenezi n’chilungamo.+
10 Mwachitsanzo, Mose ananena kuti, ‘Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako,’+ komanso anati, ‘Aliyense wonenera bambo ake kapena mayi ake zachipongwe afe ndithu.’+