Ekisodo 20:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako+ kuti masiku ako atalike m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa.+ Deuteronomo 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “‘Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako+ monga mmene Yehova Mulungu wako anakulamulira, kuti masiku ako atalike, ndi kuti zinthu zikuyendere bwino+ m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa. Mateyu 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mwachitsanzo, Mulungu ananena kuti, ‘Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako.’+ Komanso anati, ‘Aliyense wonenera bambo ake kapena mayi ake zachipongwe afe ndithu.’+ Aefeso 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako,”+ ndilo lamulo loyamba lokhala ndi lonjezo:+
12 “Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako+ kuti masiku ako atalike m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa.+
16 “‘Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako+ monga mmene Yehova Mulungu wako anakulamulira, kuti masiku ako atalike, ndi kuti zinthu zikuyendere bwino+ m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa.
4 Mwachitsanzo, Mulungu ananena kuti, ‘Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako.’+ Komanso anati, ‘Aliyense wonenera bambo ake kapena mayi ake zachipongwe afe ndithu.’+