Ekisodo 21:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Womenya abambo ake ndi mayi ake aziphedwa ndithu.+ Levitiko 19:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “‘Aliyense wa inu aziopa mayi ndi bambo ake,+ ndipo muzisunga masabata anga.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu. Deuteronomo 27:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “‘Wotembereredwa ndi munthu wonyoza bambo ake kapena mayi ake.’+ (Anthu onse ayankhe kuti, ‘Zikhale momwemo!’) Miyambo 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mwana wanga, tamvera malangizo a bambo ako,+ ndipo usasiye malamulo a mayi ako,+ Maliko 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mwachitsanzo, Mose ananena kuti, ‘Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako,’+ komanso anati, ‘Aliyense wonenera bambo ake kapena mayi ake zachipongwe afe ndithu.’+
3 “‘Aliyense wa inu aziopa mayi ndi bambo ake,+ ndipo muzisunga masabata anga.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu.
16 “‘Wotembereredwa ndi munthu wonyoza bambo ake kapena mayi ake.’+ (Anthu onse ayankhe kuti, ‘Zikhale momwemo!’)
10 Mwachitsanzo, Mose ananena kuti, ‘Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako,’+ komanso anati, ‘Aliyense wonenera bambo ake kapena mayi ake zachipongwe afe ndithu.’+