Numeri 30:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma ngati bambo ake am’kaniza pa tsiku limene amva malonjezo ake onse, malonjezo ake odzimana amene walumbirira moyo wake, akhale opanda ntchito. Yehova adzam’khululukira chifukwa bambo ake anam’kaniza.+
5 Koma ngati bambo ake am’kaniza pa tsiku limene amva malonjezo ake onse, malonjezo ake odzimana amene walumbirira moyo wake, akhale opanda ntchito. Yehova adzam’khululukira chifukwa bambo ake anam’kaniza.+