Ekisodo 25:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo mundipangire malo opatulika, popeza ndiyenera kukhala pakati panu.+ Ekisodo 29:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova Mulungu wawo, amene ndinawatulutsa m’dziko la Iguputo kuti ndikhale pakati pawo.+ Ine ndine Yehova Mulungu wawo.+ Levitiko 26:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Motero ndidzayendadi pakati panu ndi kukusonyezani kuti ine ndine Mulungu wanu,+ ndipo inu mudzakhala anthu anga.+ 1 Mafumu 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndidzakhaladi pakati pa ana a Isiraeli,+ ndipo sindidzasiya anthu anga, Aisiraeli.”+
46 Iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova Mulungu wawo, amene ndinawatulutsa m’dziko la Iguputo kuti ndikhale pakati pawo.+ Ine ndine Yehova Mulungu wawo.+
12 Motero ndidzayendadi pakati panu ndi kukusonyezani kuti ine ndine Mulungu wanu,+ ndipo inu mudzakhala anthu anga.+