-
Numeri 27:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Kenako ana aakazi a Tselofekadi+ anafika kwa Mose. Tselofekadi anali mwana wa Heferi, Heferi anali mwana wa Giliyadi, Giliyadi anali mwana wa Makiri, ndipo Makiri anali mwana wa Manase.+ Onsewa anali ochokera kumabanja a Manase mwana wa Yosefe. Ana aakazi a Tselofekadi amenewo mayina awo anali Mala, Nowa, Hogila, Milika ndi Tiriza.+
-