Ekisodo 25:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Ndiyeno upange tebulo+ la mtengo wa mthethe, mikono iwiri m’litali, mkono umodzi m’lifupi ndi mkono umodzi ndi hafu msinkhu wake. Levitiko 24:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo usanjikize mikateyo m’magulu awiri. Gulu lililonse likhale ndi mikate 6.+ Uike mikateyo patebulo lagolide woyenga bwino pamaso pa Yehova.+
23 “Ndiyeno upange tebulo+ la mtengo wa mthethe, mikono iwiri m’litali, mkono umodzi m’lifupi ndi mkono umodzi ndi hafu msinkhu wake.
6 Ndipo usanjikize mikateyo m’magulu awiri. Gulu lililonse likhale ndi mikate 6.+ Uike mikateyo patebulo lagolide woyenga bwino pamaso pa Yehova.+