Genesis 30:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Zitatero, Rakele anati: “Mulungu wakhala monga woweruza+ wanga ndipo wamvera mawu anga, choncho wandipatsa mwana wamwamuna.” N’chifukwa chake Rakele anatcha mwanayo dzina lakuti Dani.*+ Genesis 49:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Dani adzakhala njoka yobisala m’mbali mwa msewu, njoka yokhala ndi tinyanga yobisala m’mphepete mwa njira, imene imaluma chidendene cha hatchi ndipo wokwerapo amagwa chagada.+
6 Zitatero, Rakele anati: “Mulungu wakhala monga woweruza+ wanga ndipo wamvera mawu anga, choncho wandipatsa mwana wamwamuna.” N’chifukwa chake Rakele anatcha mwanayo dzina lakuti Dani.*+
17 Dani adzakhala njoka yobisala m’mbali mwa msewu, njoka yokhala ndi tinyanga yobisala m’mphepete mwa njira, imene imaluma chidendene cha hatchi ndipo wokwerapo amagwa chagada.+