37 Awa ndiwo anawerengedwa+ mwa mabanja a ana a Kohati, onse otumikira m’chihema chokumanako, amene Mose ndi Aroni anawawerenga pomvera mawu a Yehova kwa Mose.
41 Amenewa ndiwo anawerengedwa mwa mabanja a ana a Gerisoni, onse otumikira m’chihema chokumanako, amene Mose ndi Aroni anawawerenga pomvera mawu a Yehova.+