2 Mbiri 34:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “Yehova wanena kuti, ‘Ndibweretsa tsoka+ pamalo ano ndi anthu ake,+ pokwaniritsa matemberero onse+ amene analembedwa m’buku limene anawerenga pamaso pa mfumu ya Yuda,+ Yeremiya 51:60 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 60 Yeremiya analemba m’buku limodzi+ za masoka onse odzagwera Babulo. Iye analemba mawu onsewa okhudza zimene zidzachitikire Babulo.
24 “Yehova wanena kuti, ‘Ndibweretsa tsoka+ pamalo ano ndi anthu ake,+ pokwaniritsa matemberero onse+ amene analembedwa m’buku limene anawerenga pamaso pa mfumu ya Yuda,+
60 Yeremiya analemba m’buku limodzi+ za masoka onse odzagwera Babulo. Iye analemba mawu onsewa okhudza zimene zidzachitikire Babulo.