Deuteronomo 33:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Amenewa azilangiza Yakobo pa zigamulo zanu,+Ndi Isiraeli m’chilamulo chanu.+Azipereka nsembe zofukiza kuti muzinunkhiza fungo lake,+Ndi nsembe yathunthu paguwa lanu lansembe.+
10 Amenewa azilangiza Yakobo pa zigamulo zanu,+Ndi Isiraeli m’chilamulo chanu.+Azipereka nsembe zofukiza kuti muzinunkhiza fungo lake,+Ndi nsembe yathunthu paguwa lanu lansembe.+