Deuteronomo 1:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 amene anali kutsogola kuti akuzondereni malo oti mumangepo msasa wanu.+ Usiku anali kukutsogolerani ndi moto kuti muziona njira yoyendamo, ndipo masana anali kukutsogolerani ndi mtambo.+ Yoswa 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 ndipo anauza anthuwo kuti: “Mukangoona likasa la pangano la Yehova Mulungu wanu litanyamulidwa ndi ansembe achilevi,+ musamuke pamalo panu ndi kulitsatira, Yoswa 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 koma musaliyandikire. Pakati pa inu ndi likasalo pakhale mtunda wokwana mikono* pafupifupi 2,000.+ Mukatero, mudzadziwa njira yoyenera kuyendamo, pakuti kumeneko simunayambe mwapitako.”
33 amene anali kutsogola kuti akuzondereni malo oti mumangepo msasa wanu.+ Usiku anali kukutsogolerani ndi moto kuti muziona njira yoyendamo, ndipo masana anali kukutsogolerani ndi mtambo.+
3 ndipo anauza anthuwo kuti: “Mukangoona likasa la pangano la Yehova Mulungu wanu litanyamulidwa ndi ansembe achilevi,+ musamuke pamalo panu ndi kulitsatira,
4 koma musaliyandikire. Pakati pa inu ndi likasalo pakhale mtunda wokwana mikono* pafupifupi 2,000.+ Mukatero, mudzadziwa njira yoyenera kuyendamo, pakuti kumeneko simunayambe mwapitako.”