Ekisodo 13:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yehova anali kuyenda patsogolo pawo mumtambo woima njo ngati chipilala powatsogolera usana,+ ndipo usiku anali kuwatsogolera m’moto woima njo ngati chipilala kuti uziwaunikira, kuti apitirizebe ulendo usana ndi usiku.+ Ekisodo 40:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 M’zigawo zonse za ulendo wawo, mtambowo ukakwera pamwamba pa chihema chokumanako, ana a Isiraeli anali kunyamuka n’kuyamba ulendo.+ Numeri 10:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Akanyamuka pamsasa masana, mtambo wa Yehova+ unali pamwamba pawo. Nehemiya 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Usana munali kuwatsogolera ndi mtambo woima njo ngati chipilala,+ ndipo usiku munali kuwatsogolera ndi moto woima njo ngati chipilala+ kuti uziwaunikira+ njira imene anayenera kuyendamo. Salimo 78:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iye anapitiriza kuwatsogolera ndi mtambo masana,+Ndipo usiku wonse anali kuwatsogolera ndi kuwala kwa moto.+ Salimo 105:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Mulungu anayala mtambo kuti uziwatchinga,+Ndipo anawapatsa moto kuti uziwaunikira usiku.+
21 Yehova anali kuyenda patsogolo pawo mumtambo woima njo ngati chipilala powatsogolera usana,+ ndipo usiku anali kuwatsogolera m’moto woima njo ngati chipilala kuti uziwaunikira, kuti apitirizebe ulendo usana ndi usiku.+
36 M’zigawo zonse za ulendo wawo, mtambowo ukakwera pamwamba pa chihema chokumanako, ana a Isiraeli anali kunyamuka n’kuyamba ulendo.+
12 Usana munali kuwatsogolera ndi mtambo woima njo ngati chipilala,+ ndipo usiku munali kuwatsogolera ndi moto woima njo ngati chipilala+ kuti uziwaunikira+ njira imene anayenera kuyendamo.
14 Iye anapitiriza kuwatsogolera ndi mtambo masana,+Ndipo usiku wonse anali kuwatsogolera ndi kuwala kwa moto.+