Ekisodo 33:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipo Mose akangolowa m’chihema, mtambo woima njo ngati chipilala+ unali kutsika ndi kuima pakhomo la chihemacho. Zikatero Mulungu anali kulankhula+ ndi Mose. Numeri 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano Yehova anatsika mumtambo woima njo ngati chipilala+ n’kuima pakhomo la chihema chokumanako, ndipo anaitana Aroni ndi Miriamu. Pamenepo iwo anayandikira kumeneko. Deuteronomo 31:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno Yehova anaonekera kuchihemako, mumtambo woima njo ngati chipilala, ndipo mtambowo unaima pakhomo la chihema.+
9 Ndipo Mose akangolowa m’chihema, mtambo woima njo ngati chipilala+ unali kutsika ndi kuima pakhomo la chihemacho. Zikatero Mulungu anali kulankhula+ ndi Mose.
5 Tsopano Yehova anatsika mumtambo woima njo ngati chipilala+ n’kuima pakhomo la chihema chokumanako, ndipo anaitana Aroni ndi Miriamu. Pamenepo iwo anayandikira kumeneko.
15 Ndiyeno Yehova anaonekera kuchihemako, mumtambo woima njo ngati chipilala, ndipo mtambowo unaima pakhomo la chihema.+