Ekisodo 33:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipo Mose akangolowa m’chihema, mtambo woima njo ngati chipilala+ unali kutsika ndi kuima pakhomo la chihemacho. Zikatero Mulungu anali kulankhula+ ndi Mose. Ekisodo 40:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Mtambo wa Yehovawo unali kukhala pamwamba pa chihema chopatulika usana, ndipo usiku panali kukhala moto. Nyumba yonse ya Isiraeli inali kuona zimenezi m’zigawo zonse za ulendo wawo.+ Salimo 99:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mulungu anapitiriza kulankhula nawo mumtambo woima njo ngati chipilala.+Iwo anasunga zikumbutso zake ndi malangizo amene anawapatsa.+
9 Ndipo Mose akangolowa m’chihema, mtambo woima njo ngati chipilala+ unali kutsika ndi kuima pakhomo la chihemacho. Zikatero Mulungu anali kulankhula+ ndi Mose.
38 Mtambo wa Yehovawo unali kukhala pamwamba pa chihema chopatulika usana, ndipo usiku panali kukhala moto. Nyumba yonse ya Isiraeli inali kuona zimenezi m’zigawo zonse za ulendo wawo.+
7 Mulungu anapitiriza kulankhula nawo mumtambo woima njo ngati chipilala.+Iwo anasunga zikumbutso zake ndi malangizo amene anawapatsa.+