Deuteronomo 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tembenukani ndi kulowera kudera lamapiri la Aamori+ ndi anthu oyandikana nawo onse okhala ku Araba,+ kudera lamapiri,+ ku Sefela, ku Negebu,+ m’mbali mwa nyanja,+ m’dziko la Akanani+ ndi ku Lebanoni+ mpaka kumtsinje waukulu wa Firate.+ Oweruza 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako ana a Yuda anatsika kukamenyana ndi Akanani okhala m’dera lamapiri, ku Negebu+ ndi ku Sefela.+
7 Tembenukani ndi kulowera kudera lamapiri la Aamori+ ndi anthu oyandikana nawo onse okhala ku Araba,+ kudera lamapiri,+ ku Sefela, ku Negebu,+ m’mbali mwa nyanja,+ m’dziko la Akanani+ ndi ku Lebanoni+ mpaka kumtsinje waukulu wa Firate.+
9 Kenako ana a Yuda anatsika kukamenyana ndi Akanani okhala m’dera lamapiri, ku Negebu+ ndi ku Sefela.+