Numeri 13:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Atapita ku Negebu,+ anakafika ku Heburoni.+ Kumeneko anapezako Ahimani, Sesai ndi Talimai,+ mbadwa za Anaki.*+ Mzinda wa Heburoni+ unamangidwa zaka 7 mzinda wa Zowani+ wa ku Iguputo usanamangidwe. Numeri 13:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Tinaonakonso Anefili,* mbadwa za Anaki,+ moti eni akefe tinangodziona ngati tiziwala kwa iwo. Iwonso ndi mmene anationera.”+
22 Atapita ku Negebu,+ anakafika ku Heburoni.+ Kumeneko anapezako Ahimani, Sesai ndi Talimai,+ mbadwa za Anaki.*+ Mzinda wa Heburoni+ unamangidwa zaka 7 mzinda wa Zowani+ wa ku Iguputo usanamangidwe.
33 Tinaonakonso Anefili,* mbadwa za Anaki,+ moti eni akefe tinangodziona ngati tiziwala kwa iwo. Iwonso ndi mmene anationera.”+