Numeri 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “‘Koma ngati mukupereka ng’ombe yamphongo monga nsembe yopsereza,+ kapena monga nsembe yochitira lonjezo lapadera,+ kapenanso monga nsembe zachiyanjano kwa Yehova,+ Numeri 15:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiponso muzikapereka vinyo monga nsembe yachakumwa.+ Vinyoyo azikakhala wokwanira hafu ya muyezo wa hini. Akakhale nsembe yotentha ndi moto, yafungo lokhazika mtima pansi kwa Yehova.
8 “‘Koma ngati mukupereka ng’ombe yamphongo monga nsembe yopsereza,+ kapena monga nsembe yochitira lonjezo lapadera,+ kapenanso monga nsembe zachiyanjano kwa Yehova,+
10 Ndiponso muzikapereka vinyo monga nsembe yachakumwa.+ Vinyoyo azikakhala wokwanira hafu ya muyezo wa hini. Akakhale nsembe yotentha ndi moto, yafungo lokhazika mtima pansi kwa Yehova.