Deuteronomo 11:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Chotero mawu angawa muwasunge m’mitima yanu+ ndi kuwatsatira m’moyo wanu. Muwamange monga chizindikiro padzanja lanu, ndipo akhale ngati chomanga pamphumi panu.*+
18 “Chotero mawu angawa muwasunge m’mitima yanu+ ndi kuwatsatira m’moyo wanu. Muwamange monga chizindikiro padzanja lanu, ndipo akhale ngati chomanga pamphumi panu.*+