Deuteronomo 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo mawu awa amene ndikukulamula lero azikhala pamtima pako,+ Salimo 37:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Chilamulo cha Mulungu wake chili mumtima mwake.+Poyenda mapazi ake sadzaterereka.+ Miyambo 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Uwamange kuzala zako,+ ndipo uwalembe pamtima pako.+ Yesaya 51:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Ndimvereni, inu odziwa chilungamo, inu amene muli ndi lamulo langa mumtima mwanu.+ Musaope chitonzo cha anthu ndipo musachite mantha chifukwa cha mawu awo onyoza.+
7 “Ndimvereni, inu odziwa chilungamo, inu amene muli ndi lamulo langa mumtima mwanu.+ Musaope chitonzo cha anthu ndipo musachite mantha chifukwa cha mawu awo onyoza.+