Numeri 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mwa ana a Yosefe+ kuchokera ku fuko la Efuraimu,+ Elisama mwana wa Amihudi, kuchokera ku fuko la Manase,+ Gamaliyeli mwana wa Pedazuri, Numeri 7:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Pa tsiku la 7 panali mtsogoleri wa ana a Efuraimu, Elisama+ mwana wa Amihudi. Numeri 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndiyeno a m’chigawo cha mafuko atatu cha ana a Efuraimu+ ananyamuka m’magulu awo. Mtsogoleri wa asilikali awo anali Elisama,+ mwana wa Amihudi.
10 Mwa ana a Yosefe+ kuchokera ku fuko la Efuraimu,+ Elisama mwana wa Amihudi, kuchokera ku fuko la Manase,+ Gamaliyeli mwana wa Pedazuri,
22 Ndiyeno a m’chigawo cha mafuko atatu cha ana a Efuraimu+ ananyamuka m’magulu awo. Mtsogoleri wa asilikali awo anali Elisama,+ mwana wa Amihudi.