2 Samueli 22:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndidzakhalabe wopanda cholakwa+ pamaso pake,Ndipo ndidzayesetsa kupewa cholakwa.+ Salimo 37:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Yehova amadziwa za moyo wa anthu osalakwa,+Ndipo cholowa chawo chidzakhalapo mpaka kalekale.+ Mateyu 5:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Choncho khalani angwiro, monga mmene Atate wanu wakumwamba alili wangwiro.+ 2 Petulo 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chotero okondedwa, pakuti mukuyembekezera zinthu zimenezi, chitani chilichonse chotheka kuti iye adzakupezeni opanda banga,+ opanda chilema ndiponso muli mu mtendere.+
14 Chotero okondedwa, pakuti mukuyembekezera zinthu zimenezi, chitani chilichonse chotheka kuti iye adzakupezeni opanda banga,+ opanda chilema ndiponso muli mu mtendere.+