Yoswa 20:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Imeneyi inali mizinda imene inasankhidwa kuti ana a Isiraeli onse ndi alendo okhala pakati pawo, azithawirako akapha munthu mwangozi,+ kuti asaphedwe ndi wobwezera magazi mpaka akaonekere pamaso pa oweruza.+
9 Imeneyi inali mizinda imene inasankhidwa kuti ana a Isiraeli onse ndi alendo okhala pakati pawo, azithawirako akapha munthu mwangozi,+ kuti asaphedwe ndi wobwezera magazi mpaka akaonekere pamaso pa oweruza.+