Numeri 35:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mukasankhe mizinda yoyenerera kwa inu, kuti ikakhale mizinda yanu yothawirako. Munthu amene wapha mnzake mwangozi azikathawira kumeneko.+ Numeri 35:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kwa ana a Isiraeli, kwa mlendo,+ ndi kwa munthu amene wakhaliratu pakati pawo, mizinda 6 imeneyi ikakhala kothawirako aliyense amene wapha munthu mwangozi.+
11 Mukasankhe mizinda yoyenerera kwa inu, kuti ikakhale mizinda yanu yothawirako. Munthu amene wapha mnzake mwangozi azikathawira kumeneko.+
15 Kwa ana a Isiraeli, kwa mlendo,+ ndi kwa munthu amene wakhaliratu pakati pawo, mizinda 6 imeneyi ikakhala kothawirako aliyense amene wapha munthu mwangozi.+