Ekisodo 21:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma ngati sanachite kum’dikirira, ndipo Mulungu woona walola kuti mwangozi munthuyo afere m’manja mwake,+ pamenepo ndidzakukonzerani malo amene angathawireko.+ Deuteronomo 4:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 kuti munthu wopha mnzake mwangozi,+ amene sanali kudana naye kale n’kale,+ azithawirako. Ameneyu azithawira ku umodzi mwa mizinda imeneyi ndi kukhala ndi moyo.+ Deuteronomo 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Nkhani ya munthu wopha mnzake amene angathawire kumeneko kuti akhale ndi moyo, izikhala yotere: Akapha munthu mosadziwa ndipo sanali kudana naye,+
13 Koma ngati sanachite kum’dikirira, ndipo Mulungu woona walola kuti mwangozi munthuyo afere m’manja mwake,+ pamenepo ndidzakukonzerani malo amene angathawireko.+
42 kuti munthu wopha mnzake mwangozi,+ amene sanali kudana naye kale n’kale,+ azithawirako. Ameneyu azithawira ku umodzi mwa mizinda imeneyi ndi kukhala ndi moyo.+
4 “Nkhani ya munthu wopha mnzake amene angathawire kumeneko kuti akhale ndi moyo, izikhala yotere: Akapha munthu mosadziwa ndipo sanali kudana naye,+