Numeri 35:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mukasankhe mizinda yoyenerera kwa inu, kuti ikakhale mizinda yanu yothawirako. Munthu amene wapha mnzake mwangozi azikathawira kumeneko.+ Numeri 35:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “‘Koma ngati wamukankha mwangozi, osati chifukwa cha chidani, kapena ngati wam’ponyera chinachake mwangozi, osati mochita kum’bisalira,+
11 Mukasankhe mizinda yoyenerera kwa inu, kuti ikakhale mizinda yanu yothawirako. Munthu amene wapha mnzake mwangozi azikathawira kumeneko.+
22 “‘Koma ngati wamukankha mwangozi, osati chifukwa cha chidani, kapena ngati wam’ponyera chinachake mwangozi, osati mochita kum’bisalira,+