Salimo 145:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova amakomera mtima aliyense,+Ndipo ntchito zake zonse amazichitira chifundo.+ Mlaliki 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 komanso kuti munthu aliyense adye ndi kumwa ndi kusangalala ndi zinthu zabwino, chifukwa choti wagwira ntchito mwakhama.+ Imeneyi ndi mphatso yochokera kwa Mulungu.+
13 komanso kuti munthu aliyense adye ndi kumwa ndi kusangalala ndi zinthu zabwino, chifukwa choti wagwira ntchito mwakhama.+ Imeneyi ndi mphatso yochokera kwa Mulungu.+