Genesis 49:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Rubeni, iwe ndiwe mwana wanga woyamba kubadwa,+ nyonga yanga ndi poyambira mphamvu zanga zobereka.+ Unayenera kukhala ndi ulemu wopambana ndi mphamvu zopambana. Salimo 105:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Mulungu anapha mwana aliyense woyamba kubadwa m’dziko lawo,+Chiyambi cha mphamvu zawo zonse zobereka.+
3 “Rubeni, iwe ndiwe mwana wanga woyamba kubadwa,+ nyonga yanga ndi poyambira mphamvu zanga zobereka.+ Unayenera kukhala ndi ulemu wopambana ndi mphamvu zopambana.
36 Mulungu anapha mwana aliyense woyamba kubadwa m’dziko lawo,+Chiyambi cha mphamvu zawo zonse zobereka.+