Genesis 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 ndi Ahori+ kuphiri lawo la Seiri,+ mpaka kukafika ku Eli-parana,+ kuchipululu. Genesis 36:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Nawa ana a Seiri Mhori, eni dzikolo:+ Lotani, Sobala, Zibeoni, Ana,+ 1 Mbiri 1:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Ana a Lotani anali Hori ndi Homamu. Mlongo wake wa Lotani anali Timina.+