Deuteronomo 25:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ngati woipayo akuyenera kukwapulidwa,+ woweruza azilamula kuti woipayo amugoneke pansi, ndipo azim’kwapula+ pamaso pa woweruzayo. Azimukwapula zikoti zogwirizana ndi choipa chimene wachita. Miyambo 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamilomo ya munthu womvetsa zinthu pamapezeka nzeru,+ koma ndodo amakwapulira msana wa munthu wopanda nzeru mumtima mwake.+ Miyambo 19:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Zilango anazikhazikitsira anthu onyoza,+ ndipo zikwapu anazisungira msana wa anthu opusa.+ Miyambo 20:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Zilonda zobwera chifukwa chomenyedwa zimachotsa zoipa,+ ndipo zikwapu zimafika mpaka mkatikati mwa mimba.+
2 Ngati woipayo akuyenera kukwapulidwa,+ woweruza azilamula kuti woipayo amugoneke pansi, ndipo azim’kwapula+ pamaso pa woweruzayo. Azimukwapula zikoti zogwirizana ndi choipa chimene wachita.
13 Pamilomo ya munthu womvetsa zinthu pamapezeka nzeru,+ koma ndodo amakwapulira msana wa munthu wopanda nzeru mumtima mwake.+
30 Zilonda zobwera chifukwa chomenyedwa zimachotsa zoipa,+ ndipo zikwapu zimafika mpaka mkatikati mwa mimba.+