Genesis 27:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Koma Isaki bambo ake anamuuza kuti: “Taona, udzakhala kutali ndi nthaka yachonde, kotalikirana ndi mame akumwamba.+ Genesis 27:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Udzakhalira moyo lupanga+ ndipo udzatumikira m’bale wako.+ Koma ukadzatopa ndi goli lake, udzalithyola ndi kulichotsa m’khosi mwako.”+
39 Koma Isaki bambo ake anamuuza kuti: “Taona, udzakhala kutali ndi nthaka yachonde, kotalikirana ndi mame akumwamba.+
40 Udzakhalira moyo lupanga+ ndipo udzatumikira m’bale wako.+ Koma ukadzatopa ndi goli lake, udzalithyola ndi kulichotsa m’khosi mwako.”+