Salimo 107:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Mulungu amawadalitsa moti amachuluka kwambiri,+Ndipo salola kuti ng’ombe zawo zikhale zochepa.+