1 Samueli 17:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Iye anapitiriza kuuza Davide kuti: “Tangoyerekeza kubwera kuno, ndipereka mnofu wako kwa mbalame zam’mlengalenga ndi kwa zilombo zakutchire.”+ Salimo 79:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Apereka mitembo ya atumiki anu kwa mbalame kuti chikhale chakudya chawo.+Matupi a okhulupirika anu awapereka kwa zilombo zakutchire.+ Yeremiya 7:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Mitembo ya anthu awa idzakhala chakudya cha zolengedwa zouluka zam’mlengalenga ndi cha zilombo zakutchire, ndipo sipadzakhala woziopsa.+
44 Iye anapitiriza kuuza Davide kuti: “Tangoyerekeza kubwera kuno, ndipereka mnofu wako kwa mbalame zam’mlengalenga ndi kwa zilombo zakutchire.”+
2 Apereka mitembo ya atumiki anu kwa mbalame kuti chikhale chakudya chawo.+Matupi a okhulupirika anu awapereka kwa zilombo zakutchire.+
33 Mitembo ya anthu awa idzakhala chakudya cha zolengedwa zouluka zam’mlengalenga ndi cha zilombo zakutchire, ndipo sipadzakhala woziopsa.+