Deuteronomo 29:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 kuti muchite pangano+ ndi Yehova Mulungu wanu mwa kulumbira, pangano limene Yehova Mulungu wanu akuchita nanu lero.+
12 kuti muchite pangano+ ndi Yehova Mulungu wanu mwa kulumbira, pangano limene Yehova Mulungu wanu akuchita nanu lero.+