1 Mafumu 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nyumba iyi idzakhala bwinja.+ Aliyense wodutsa pafupi nayo adzayang’ana modabwa+ ndi kuimba mluzu n’kunena kuti, ‘N’chifukwa chiyani Yehova anachita zimenezi padzikoli ndi panyumbayi?’+ 2 Mbiri 7:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndipo nyumba iyi ikadzakhala bwinja,+ aliyense wodutsa pafupi nayo adzayang’ana modabwa,+ ndipo ndithu adzati, ‘N’chifukwa chiyani Yehova anachita zimenezi padzikoli ndi panyumbayi?’+ Yeremiya 22:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anthu a mitundu yambiri adzadutsa pafupi ndi mzinda uwu ndipo adzafunsana kuti: “N’chifukwa chiyani Yehova anachitira mzinda waukuluwu zinthu zoterezi?”+
8 Nyumba iyi idzakhala bwinja.+ Aliyense wodutsa pafupi nayo adzayang’ana modabwa+ ndi kuimba mluzu n’kunena kuti, ‘N’chifukwa chiyani Yehova anachita zimenezi padzikoli ndi panyumbayi?’+
21 Ndipo nyumba iyi ikadzakhala bwinja,+ aliyense wodutsa pafupi nayo adzayang’ana modabwa,+ ndipo ndithu adzati, ‘N’chifukwa chiyani Yehova anachita zimenezi padzikoli ndi panyumbayi?’+
8 Anthu a mitundu yambiri adzadutsa pafupi ndi mzinda uwu ndipo adzafunsana kuti: “N’chifukwa chiyani Yehova anachitira mzinda waukuluwu zinthu zoterezi?”+