Deuteronomo 11:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 ndipo mudzalandira temberero+ limeneli ngati simudzamvera malamulo a Yehova Mulungu wanu,+ n’kupatuka panjira imene ndikukulamulani lero kuti muziyendamo, n’kuyamba kutsatira milungu ina imene simukuidziwa. Deuteronomo 28:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Mukapanda kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu ndi kuonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse ndi mfundo zake zimene ndikukupatsani lero, matemberero otsatirawa adzakugwerani ndi kukupezani:+
28 ndipo mudzalandira temberero+ limeneli ngati simudzamvera malamulo a Yehova Mulungu wanu,+ n’kupatuka panjira imene ndikukulamulani lero kuti muziyendamo, n’kuyamba kutsatira milungu ina imene simukuidziwa.
15 “Mukapanda kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu ndi kuonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse ndi mfundo zake zimene ndikukupatsani lero, matemberero otsatirawa adzakugwerani ndi kukupezani:+