Aroma 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma adzapereka chilango ndi mkwiyo+ kwa okonda mikangano+ amenenso samvera choonadi+ koma amamvera zosalungama. Aroma 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Aliyense wochita zoipa, kuyambira Myuda+ mpaka Mgiriki,+ adzaona nsautso ndi zowawa.
8 Koma adzapereka chilango ndi mkwiyo+ kwa okonda mikangano+ amenenso samvera choonadi+ koma amamvera zosalungama.