Deuteronomo 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti iye ndi amene Yehova Mulungu wako wam’sankha pakati pa mafuko anu onse, kuti iye pamodzi ndi ana ake aimirire ndi kutumikira m’dzina la Yehova nthawi zonse.+ Malaki 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Lamulo la choonadi linali m’kamwa mwake+ ndipo pamilomo pake panalibe zosalungama. Anali kuyenda ndi ine mwamtendere komanso mowongoka mtima,+ ndipo anabweza anthu ambiri panjira zawo zolakwika.+
5 Pakuti iye ndi amene Yehova Mulungu wako wam’sankha pakati pa mafuko anu onse, kuti iye pamodzi ndi ana ake aimirire ndi kutumikira m’dzina la Yehova nthawi zonse.+
6 Lamulo la choonadi linali m’kamwa mwake+ ndipo pamilomo pake panalibe zosalungama. Anali kuyenda ndi ine mwamtendere komanso mowongoka mtima,+ ndipo anabweza anthu ambiri panjira zawo zolakwika.+